Posts

Image
  By Reporter   Donald Trump ndiye wasankhidwa kukhala msogoleri wachinamba 47 wa dziko la Amerika. A Trump apeza ma voti opyola 270 omwe ndi mlingo opambanila utsogoleri mdzikomo. Atsogoleri amayiko ena ayamba kale kufunila zabwino a Trump,ena mwa tsogoleri wa ndi Vladmir Putin wa dziko la Russia,Xi Jinping waku China ndi ena. A Trump ali ndi mfundo zawo monga kusagwirizana ndi nchitidwe wokwatirana amuna kapena akazi okha okha.
Image
By Reporter  The Tobacco Commission has licensed farmers to produce 223 million kilogrammes for the next growing season which represents a 25% increase compared to volumes licensed by this time last year.  The demand for last year was at 190 million kgs but the country only supplied 133 million kgs. Tobacco Commission described the lower production as a missed opportunity for tobacco growers considering the prices that were offered Grower licensing which started in June will close on October 31.  Tobacco remains Malawis main export crop with this year’s sales of $396.28 million,up from $283.76 the previous year