Posts

Showing posts from March, 2025
Image
  Malawi national team Head Coach Kalisto Pasuwa has named a 28-man squad for the forthcoming 2026 FIFA World Cup qualifiers against Namibia and Tunisia. Malawi will host Namibia at Bingu National Stadium on Thursday March 20 before flying out to Tunis to face group leaders Tunisia on March 24. The flames is in group H and currently on position 4 with Tunisia,Namibia and Liberia ahead in that order.  
Image
 Akulu akulu ena ama kampani aboma monga mkulu oyang’anila kampani ya Malawi Energy Regulatory Authority a Henry Kachaje ndi mkulu wa National Oil Company of Malawi a Clement Kanyama ali mdziko la United Arab Emirates kokakambilana ndima kampani ena ogulitsa mafuta ammayiko aluya.   Gululi lomwe latsogozedwa ndi mlembi mu unduna wazamphamvu engineer Alfonso Chikuni, dzulo anakambilana ndi akuluakulu ena a dziko la Oman lomwe ndi limodzi mwamayiko oyenga mafuta.  Ulendowu wadza malinga ndi malingaliro aboma ofuna kumagula mafuta munjira ya boma ndi boma (government to government).  Mu december chaka chatha mtsogoleri wadziko lino Lazarus Chakwera analinso mdziko la United Arab Emirates kukapanganso migwirizano yonga yomweyi.                       Muchinthunzi: Nthumwizi