By Reporter

 Donald Trump ndiye wasankhidwa kukhala msogoleri wachinamba 47 wa dziko la Amerika.

A Trump apeza ma voti opyola 270 omwe ndi mlingo opambanila utsogoleri mdzikomo.

Atsogoleri amayiko ena ayamba kale kufunila zabwino a Trump,ena mwa tsogoleri wa ndi Vladmir Putin wa dziko la Russia,Xi Jinping waku China ndi ena.

A Trump ali ndi mfundo zawo monga kusagwirizana ndi nchitidwe wokwatirana amuna kapena akazi okha okha.

Comments

Popular posts from this blog